Malawi Legal Aid Bureau (@mwlegalaid) 's Twitter Profile
Malawi Legal Aid Bureau

@mwlegalaid

Legal Aid Bureau's role is to ensure that poor people have access to justice and legal remedies as provided for under section 41 of the Constitution.

ID: 1347170186269495299

linkhttp://www.legalaidbureau.org calendar_today07-01-2021 13:18:19

1,1K Tweet

1,1K Followers

106 Following

Malawi Legal Aid Bureau (@mwlegalaid) 's Twitter Profile Photo

𝐖𝐄 𝐀𝐑𝐄 π‡πˆπ‘πˆππ†! Vacant posts available are: 3 Senior Legal Aid Advocates (Grade H), 3 Drivers (Grade N), 8 Process Servers (Grade P). You can get a full description of the vacancies on our website: bit.ly/44BXPKC

𝐖𝐄 𝐀𝐑𝐄 π‡πˆπ‘πˆππ†!

Vacant posts available are:

3 Senior Legal Aid Advocates (Grade H), 3 Drivers (Grade N), 8 Process Servers (Grade P).

You can get a full description of the vacancies on our website: bit.ly/44BXPKC
Malawi Legal Aid Bureau (@mwlegalaid) 's Twitter Profile Photo

Mdziko muno, kagawidwe ka chuma cha masiye ndi kotetezedwa ndi malamulo. Ngati mumakhala ndi mafunso ochuluka okhudza nkhani zotere, Senior Legal Aid Advocate Gift Somba akutambasula zambiri mu pulogalamu yomwe amacheza ndi MBC TV. youtu.be/jvw03YJMsOo

Mdziko muno, kagawidwe ka chuma cha masiye ndi kotetezedwa ndi malamulo. 

Ngati mumakhala ndi mafunso ochuluka okhudza nkhani zotere, Senior Legal Aid Advocate Gift Somba akutambasula zambiri mu pulogalamu yomwe amacheza ndi MBC TV.

youtu.be/jvw03YJMsOo
Malawi Legal Aid Bureau (@mwlegalaid) 's Twitter Profile Photo

Musavutike kufunsa ena za komwe kuli office ya Legal Aid Bureau m'boma lanu. Malo onse omwe tiliko alembedwa mchithunzi ichi. #LegalAid #Malawi

Musavutike kufunsa ena za komwe kuli office ya Legal Aid Bureau m'boma lanu. Malo onse omwe tiliko alembedwa mchithunzi ichi.

#LegalAid #Malawi